Miyambo 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Milomo ya anzeru imafalitsa zimene ikudziwa,+ koma mtima wa anthu opusa suchita zimenezo.+