Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 37:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Pakamwa pa munthu wolungama pamalankhula zinthu zanzeru,+

      Ndipo lilime lake limalankhula zinthu zachilungamo.+

  • Mateyu 10:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Zimene ndimakuuzani mu mdima, muzinene poyera, ndipo zimene mumamva anthu akunong’onezana, muzilalikire pamadenga.+

  • Aroma 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Munthu amakhala ndi chikhulupiriro mumtima mwake+ kuti akhale wolungama, koma ndi pakamwa pake amalengeza poyera+ chikhulupiriro chake kuti apulumuke.

  • 2 Timoteyo 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Zinthu zimene unazimva kwa ine ndi kwa mboni zambiri+ zokhudza ine, zimenezo uziphunzitse kwa anthu okhulupirika amene nawonso, adzakhala oyenerera bwino kuphunzitsa ena.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena