Yoswa 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Buku la malamulo ili lisachoke pakamwa pako,+ uziliwerenga ndi kusinkhasinkha usana ndi usiku, kuti uonetsetse kuti ukutsatira zonse zolembedwamo.+ Pakuti ukatero, udzakhala ndi moyo wopambana, ndipo udzachita zinthu mwanzeru.+ Salimo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma amakondwera ndi chilamulo cha Yehova,+Ndipo amawerenga ndi kusinkhasinkha chilamulo chake usana ndi usiku.+
8 Buku la malamulo ili lisachoke pakamwa pako,+ uziliwerenga ndi kusinkhasinkha usana ndi usiku, kuti uonetsetse kuti ukutsatira zonse zolembedwamo.+ Pakuti ukatero, udzakhala ndi moyo wopambana, ndipo udzachita zinthu mwanzeru.+
2 Koma amakondwera ndi chilamulo cha Yehova,+Ndipo amawerenga ndi kusinkhasinkha chilamulo chake usana ndi usiku.+