1 Mbiri 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zinthu zidzakuyendera bwino+ ukayesetsa kutsatira malamulo+ ndi zigamulo+ zimene Yehova analamula+ Mose zokhudza Isiraeli. Khala wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu.+ Usaope+ kapena kuchita mantha.+
13 Zinthu zidzakuyendera bwino+ ukayesetsa kutsatira malamulo+ ndi zigamulo+ zimene Yehova analamula+ Mose zokhudza Isiraeli. Khala wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu.+ Usaope+ kapena kuchita mantha.+