1 Mafumu 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Odala anthu anu,+ odala+ atumiki anuwa amene amatumikira pamaso panu nthawi zonse, n’kumamva nzeru zanu.+ Yobu 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aliyense wofuna kugwa, mawu ako anali kumudzutsa,+Ndipo mawondo olobodoka unali kuwachirikiza.+ Salimo 37:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pakamwa pa munthu wolungama pamalankhula zinthu zanzeru,+Ndipo lilime lake limalankhula zinthu zachilungamo.+ Miyambo 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Milomo ya wolungama imaweta anthu ambiri,+ koma zitsiru zimafa chifukwa chopanda nzeru mumtima.+ Luka 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamenepo onse anayamba kumutamanda ndi kudabwa ndi mawu ogwira mtima+ otuluka pakamwa pake, mwakuti anali kunena kuti: “Kodi iyeyu si mwana wa Yosefe?”+ Aefeso 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mawu alionse owola asatuluke pakamwa panu,+ koma alionse olimbikitsa monga mmene kungafunikire, kuti asangalatse owamva.+
8 Odala anthu anu,+ odala+ atumiki anuwa amene amatumikira pamaso panu nthawi zonse, n’kumamva nzeru zanu.+
30 Pakamwa pa munthu wolungama pamalankhula zinthu zanzeru,+Ndipo lilime lake limalankhula zinthu zachilungamo.+
22 Pamenepo onse anayamba kumutamanda ndi kudabwa ndi mawu ogwira mtima+ otuluka pakamwa pake, mwakuti anali kunena kuti: “Kodi iyeyu si mwana wa Yosefe?”+
29 Mawu alionse owola asatuluke pakamwa panu,+ koma alionse olimbikitsa monga mmene kungafunikire, kuti asangalatse owamva.+