Miyambo 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nzeru za munthu wochenjera ndizo kuzindikira njira imene akuyendamo,+ koma kuganiza mopusa kwa zitsiru ndi chinyengo.+ Miyambo 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munthu amene sadziwa zinthu amakhulupirira mawu alionse,+ koma wochenjera amaganizira za mmene akuyendera.+ Miyambo 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu osadziwa zinthu, ndithu adzakhala opusa,+ koma kwa ochenjera, kudziwa zinthu kudzakhala ngati chovala cha kumutu.+ Mateyu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+
8 Nzeru za munthu wochenjera ndizo kuzindikira njira imene akuyendamo,+ koma kuganiza mopusa kwa zitsiru ndi chinyengo.+
15 Munthu amene sadziwa zinthu amakhulupirira mawu alionse,+ koma wochenjera amaganizira za mmene akuyendera.+
18 Anthu osadziwa zinthu, ndithu adzakhala opusa,+ koma kwa ochenjera, kudziwa zinthu kudzakhala ngati chovala cha kumutu.+
16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+