Salimo 141:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza kukoma mtima kosatha,+Ndipo akandidzudzula ndiye kuti wandidzoza mafuta pamutu panga,+Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+Pakuti ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.+ Miyambo 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 ndipo zidzatanthauza moyo kwa iwe+ komanso zidzakhala chokongoletsa m’khosi mwako.+ Miyambo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zidzaika nkhata yamaluwa yokongola kumutu kwako.+ Zidzakuveka chisoti chachifumu chokongola.”+
5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza kukoma mtima kosatha,+Ndipo akandidzudzula ndiye kuti wandidzoza mafuta pamutu panga,+Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+Pakuti ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.+