Miyambo 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Imvi ndizo chisoti chachifumu cha ulemerero+ zikapezeka m’njira yachilungamo.+ Luka 10:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Komatu zinthu zofunika kwenikweni n’zochepa+ chabe, mwinanso n’chimodzi chokha basi. Kumbali yake, Mariya wasankha chinthu chabwino kwambiri,+ ndipo sadzalandidwa chinthu chimenechi.”
42 Komatu zinthu zofunika kwenikweni n’zochepa+ chabe, mwinanso n’chimodzi chokha basi. Kumbali yake, Mariya wasankha chinthu chabwino kwambiri,+ ndipo sadzalandidwa chinthu chimenechi.”