Miyambo 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu woipa amapeza malipiro achinyengo,+ koma wofesa chilungamo amapeza malipiro enieni.+ Miyambo 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pali njira yooneka ngati yowongoka kwa munthu,+ koma mapeto ake ndi imfa.+ Luka 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo ndidzauza+ moyo wanga kuti: “Moyo wangawe, uli ndi zinthu zambiri zabwino mwakuti zisungika kwa zaka zambiri. Ungoti phee tsopano, ndipo udye, umwe ndi kusangalala.”’+ 1 Akorinto 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi wanzeru ali kuti? Mlembi ali kuti?+ Katswiri wa mtsutso+ wa nthawi* ino ali kuti?+ Kodi Mulungu sanapange nzeru za dzikoli kukhala zopusa?+
19 Ndipo ndidzauza+ moyo wanga kuti: “Moyo wangawe, uli ndi zinthu zambiri zabwino mwakuti zisungika kwa zaka zambiri. Ungoti phee tsopano, ndipo udye, umwe ndi kusangalala.”’+
20 Kodi wanzeru ali kuti? Mlembi ali kuti?+ Katswiri wa mtsutso+ wa nthawi* ino ali kuti?+ Kodi Mulungu sanapange nzeru za dzikoli kukhala zopusa?+