Miyambo 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pali m’badwo umene umadziona kuti ndi woyera,+ koma sunasambe kuti uchotse ndowe zake.+