Miyambo 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pali njira yooneka ngati yowongoka kwa munthu,+ koma mapeto ake ndi imfa.+ Aroma 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kodi pa nthawiyo munali kukhala ndi zipatso zotani?+ Zinali zinthu+ zimene tsopano mumachita nazo manyazi. Ndipo pothera pake pa zinthu zimenezo ndi imfa.+
21 Kodi pa nthawiyo munali kukhala ndi zipatso zotani?+ Zinali zinthu+ zimene tsopano mumachita nazo manyazi. Ndipo pothera pake pa zinthu zimenezo ndi imfa.+