Miyambo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma zotsatirapo zochokera kwa iye n’zowawa kwambiri ngati chitsamba chowawa.+ N’zakuthwa ngati lupanga lakuthwa konsekonse.+ Miyambo 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pali njira yooneka ngati yowongoka kwa munthu,+ koma mapeto ake ndi imfa.+
4 Koma zotsatirapo zochokera kwa iye n’zowawa kwambiri ngati chitsamba chowawa.+ N’zakuthwa ngati lupanga lakuthwa konsekonse.+