Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 7:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ambiri adzati kwa ine pa tsiku limenelo, ‘Ambuye, Ambuye,+ kodi ife sitinalosere m’dzina lanu, ndi kutulutsa ziwanda m’dzina lanu, ndiponso kuchita ntchito zambiri zamphamvu m’dzina lanunso?’+

  • Yohane 9:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Yesu anati: “Mukanakhala akhungu, simukanakhala ndi tchimo. Koma popeza mukunena kuti, ‘Tikuona.’+ Tchimo+ lanu likhalabe chikhalire.”

  • Yohane 16:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anthu adzakuchotsani m’sunagoge.+ Ndipo nthawi ikubwera pamene aliyense wakupha inu adzaganiza kuti wachita utumiki wopatulika kwa Mulungu.+

  • Machitidwe 26:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Inetu ndinali kuganiza mumtima mwanga kuti ndiyenera kuchita zambiri zotsutsana ndi dzina la Yesu Mnazareti.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena