Salimo 59:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Taonani! Amabwetuka ndi pakamwa pawo.+Milomo yawo ili ngati malupanga,+Pakuti iwo amati: “Ndani akumvetsera?”+ Yakobo 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakamwa pamodzimodzipo pamatuluka mawu otamanda ndi otemberera. N’kosayenera abale anga kuti zinthu zimenezi zipitirire kuchitika motere.+
7 Taonani! Amabwetuka ndi pakamwa pawo.+Milomo yawo ili ngati malupanga,+Pakuti iwo amati: “Ndani akumvetsera?”+
10 Pakamwa pamodzimodzipo pamatuluka mawu otamanda ndi otemberera. N’kosayenera abale anga kuti zinthu zimenezi zipitirire kuchitika motere.+