Miyambo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nzeru zikalowa mumtima mwako,+ ndipo kudziwa zinthu kukakhala kosangalatsa m’moyo wako,+ Miyambo 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Landirani malangizo* anga osati siliva, ndiponso kudziwa zinthu m’malo mwa golide wabwino kwambiri.+
10 Landirani malangizo* anga osati siliva, ndiponso kudziwa zinthu m’malo mwa golide wabwino kwambiri.+