2 Samueli 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma Davide anayankha Rekabu ndi m’bale wake Bana, ana a Rimoni Mbeeroti kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ amene anawombola+ moyo wanga+ m’masautso anga onse,+ Mateyu 12:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pakuti ndi mawu ako udzaweruzidwa kuti ndiwe wolungama, ndipo ndi mawu akonso udzaweruzidwa kuti ndiwe wolakwa.”+ 2 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+
9 Koma Davide anayankha Rekabu ndi m’bale wake Bana, ana a Rimoni Mbeeroti kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ amene anawombola+ moyo wanga+ m’masautso anga onse,+
37 Pakuti ndi mawu ako udzaweruzidwa kuti ndiwe wolungama, ndipo ndi mawu akonso udzaweruzidwa kuti ndiwe wolakwa.”+
9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+