Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 2:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mfumu Solomo itatero, inalumbira pamaso pa Yehova kuti: “Mulungu andilange mowirikiza+ ngati Adoniya sanaike moyo wake pangozi mwa kupempha zimenezi.+

  • Salimo 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Mudzawononga olankhula bodza.+

      Munthu wokhetsa magazi+ ndi wachinyengo,+ Yehova amaipidwa naye.

  • Mlaliki 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Usalole kuti pakamwa pako pakuchimwitse,+ komanso usamanene kwa mngelo+ kuti unalakwitsa.+ Kodi Mulungu woona akwiyirenji chifukwa cha mawu ako n’kuwononga ntchito ya manja ako?+

  • Danieli 6:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Zitatero, mfumu inalamula kuti abweretse amuna amphamvu amene ananenera Danieli zoipa aja,+ ndipo anawabweretsadi. Kenako anawaponya m’dzenje la mikango+ pamodzi ndi ana awo ndi akazi awo.+ Iwo asanafike n’komwe pansi pa dzenjelo, mikango inawakhadzulakhadzula ndi kuphwanya mafupa awo onse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena