-
Yoswa 7:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Tsopano Yoswa ndi Aisiraeli onse anatenga Akani+ mwana wa Zera, limodzi ndi siliva uja, chovala chamtengo wapatali chija, mtanda wa golide uja,+ komanso ana ake aamuna ndi aakazi, ng’ombe zake, abulu, nkhosa, ndiponso hema wake, ndi chilichonse chomwe chinali chake, n’kutsikira nawo kuchigwa cha Akori.+
-