Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 15:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Anakafika ku Debiri kuchigwa cha Akori+ n’kukhotera kumpoto cha ku Giligala,+ patsogolo pa chitunda cha Adumi, kum’mwera kwa chigwa cha mtsinje. Malirewo anapitirira n’kukafika kumadzi a Eni-semesi,+ n’kukathera ku Eni-rogeli.+

  • Yesaya 65:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Sharoni+ adzakhala malo odyetserapo nkhosa.+ Chigwa cha Akori+ chidzakhala malo opumulirapo ng’ombe za anthu anga amene andifunafuna.+

  • Hoseya 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kuyambira nthawi imeneyo mpaka m’tsogolo ndidzamupatsa minda yake ya mpesa.+ Ndidzamupatsanso chigwa cha Akori+ kuti chikhale ngati khomo lachiyembekezo. Pamenepo adzayankha ngati mmene anali kuyankhira ali mtsikana,+ ngatinso mmene anayankhira pa tsiku limene anatuluka m’dziko la Iguputo.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena