Yoswa 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pambuyo pake, anaunjika mulu waukulu wa miyala pa iye. Muluwo ulipo mpaka lero.+ Zitatero, mkwiyo waukulu wa Yehova unatha.+ Ndiye chifukwa chake malowo anatchedwa chigwa cha Akori*+ mpaka lero. Yesaya 65:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sharoni+ adzakhala malo odyetserapo nkhosa.+ Chigwa cha Akori+ chidzakhala malo opumulirapo ng’ombe za anthu anga amene andifunafuna.+
26 Pambuyo pake, anaunjika mulu waukulu wa miyala pa iye. Muluwo ulipo mpaka lero.+ Zitatero, mkwiyo waukulu wa Yehova unatha.+ Ndiye chifukwa chake malowo anatchedwa chigwa cha Akori*+ mpaka lero.
10 Sharoni+ adzakhala malo odyetserapo nkhosa.+ Chigwa cha Akori+ chidzakhala malo opumulirapo ng’ombe za anthu anga amene andifunafuna.+