Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 8:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ndipo mfumu ya Ai+ anaipachika pamtengo mpaka madzulo.+ Koma dzuwa litatsala pang’ono kulowa, Yoswa analamula kuti achotse mtembo wa mfumuyo+ pamtengopo. Atauchotsa mtembowo anakauponya pachipata cha mzindawo, n’kuufotsera ndi mulu waukulu wa miyala, ndipo muluwo ulipo mpaka lero.

  • Yoswa 10:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Dzuwa likulowa, Yoswa analamula kuti atsitse mafumuwo pamitengoyo+ n’kuwaponyera m’phanga limene anabisalamo lija, ndipo anthuwo anachitadi zimenezi. Kenako anaika miyala ikuluikulu pakhomo la phangalo, yomwe ilipobe mpaka lero.

  • 2 Samueli 18:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pamapeto pake anatenga Abisalomu ndi kum’ponya m’dzenje lalikulu m’nkhalangomo ndipo anamuunjikira mulu waukulu kwambiri wa miyala.+ Koma Aisiraeli onse, aliyense anathawira kunyumba yake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena