Salimo 54:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye adzabwezera zoipa kwa adani anga.+Achititseni kukhala chete chifukwa cha choonadi chanu.+ Yesaya 38:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndadzitonthoza mpaka m’mawa.+Mafupa anga onse, iye akungokhalira kuwaphwanya ngati mkango.+Kuyambira m’mawa mpaka usiku mukungokhalira kundipereka ku zowawa.+
13 Ndadzitonthoza mpaka m’mawa.+Mafupa anga onse, iye akungokhalira kuwaphwanya ngati mkango.+Kuyambira m’mawa mpaka usiku mukungokhalira kundipereka ku zowawa.+