Salimo 39:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndichotsereni mliri umene mwandigwetsera.+Ine ndatha chifukwa cha ukali wa dzanja lanu.+