Yobu 9:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iye achotse ndodo yake pa ine,+Ndipo kuopsa kwake kusandichititse mantha. Yobu 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ikani dzanja lanu kutali ndi ine,Ndipo kuopsa kwanu kusandichititse mantha.+