Deuteronomo 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 muziichitira zimene inafuna kuti zichitikire m’bale wakezo,+ ndipo muzichotsa woipayo pakati panu.+ Esitere 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho anapachika Hamani pamtengo+ umene anakonzera Moredekai,+ ndipo mkwiyo wa mfumu unatha. Miyambo 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wolungama ndi amene amapulumutsidwa ku zowawa,+ ndipo woipa amalowa m’malo mwake.+
19 muziichitira zimene inafuna kuti zichitikire m’bale wakezo,+ ndipo muzichotsa woipayo pakati panu.+