Deuteronomo 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamenepo amuna onse a mumzinda wawo azim’ponya miyala ndi kumupha. Muzichotsa woipayo pakati panu, ndipo Aisiraeli onse adzamva ndi kuchita mantha kwambiri.+ Deuteronomo 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Munthu akaba+ mmodzi mwa abale ake, ana a Isiraeli, n’kumuchitira nkhanza ndiponso kum’gulitsa,+ wakuba munthuyo afe ndithu. Muzichotsa woipayo pakati panu.+ 1 Akorinto 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ndipo Mulungu amaweruza amene ali kunja?+ “M’chotseni pakati panu munthu woipayo.”+
21 Pamenepo amuna onse a mumzinda wawo azim’ponya miyala ndi kumupha. Muzichotsa woipayo pakati panu, ndipo Aisiraeli onse adzamva ndi kuchita mantha kwambiri.+
7 “Munthu akaba+ mmodzi mwa abale ake, ana a Isiraeli, n’kumuchitira nkhanza ndiponso kum’gulitsa,+ wakuba munthuyo afe ndithu. Muzichotsa woipayo pakati panu.+