Genesis 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chotero anam’pitikitsa munthuyo. Ndiyeno anaika akerubi+ kum’mawa kwa munda wa Edeniwo.+ Anaikanso lupanga loyaka moto, limene linali kuzungulira mosalekeza, kutchinga njira yopita ku mtengo wa moyo. Deuteronomo 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dzanja la mbonizo lizikhala loyamba kum’ponya miyala kuti afe, ndipo anthu ena onse azibwera pambuyo.+ Choncho muzichotsa woipayo pakati panu.+ Tito 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu wolimbikitsa mpatuko,+ usagwirizane+ nayenso utamudzudzula koyamba ndi kachiwiri,+ 2 Yohane 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wina akabwera kwa inu ndi chiphunzitso chosiyana ndi ichi, musamulandire m’nyumba zanu+ kapena kumupatsa moni.+
24 Chotero anam’pitikitsa munthuyo. Ndiyeno anaika akerubi+ kum’mawa kwa munda wa Edeniwo.+ Anaikanso lupanga loyaka moto, limene linali kuzungulira mosalekeza, kutchinga njira yopita ku mtengo wa moyo.
7 Dzanja la mbonizo lizikhala loyamba kum’ponya miyala kuti afe, ndipo anthu ena onse azibwera pambuyo.+ Choncho muzichotsa woipayo pakati panu.+
10 Wina akabwera kwa inu ndi chiphunzitso chosiyana ndi ichi, musamulandire m’nyumba zanu+ kapena kumupatsa moni.+