Deuteronomo 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 muzitulutsira mwamuna kapena mkazi wochita chinthu choipayo kunja kwa mzinda, ndipo muzim’ponya miyala kuti afe.+ Aroma 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano ndikukudandaulirani abale, kuti musamale ndi anthu amene amayambitsa magawano+ ndi kuchita zinthu zokhumudwitsa ena. Zimenezi ndi zosemphana ndi chiphunzitso+ chimene munaphunzira, choncho muziwapewa.+ 1 Akorinto 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma tsopano ndikukulemberani kuti muleke kuyanjana+ ndi aliyense wotchedwa m’bale, amene ndi wadama, kapena waumbombo,+ kapena wopembedza mafano, wolalata, chidakwa,+ kapena wolanda, ngakhale kudya naye munthu wotereyu ayi. 2 Atesalonika 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano tikukulangizani+ abale m’dzina la Ambuye Yesu Khristu, kuti mupewe+ m’bale aliyense woyenda mosalongosoka+ komanso mosagwirizana ndi mwambo umene tinakupatsani.+ 2 Atesalonika 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ngati wina sakumvera mawu athu+ a m’kalatayi, muikeni chizindikiro+ ndipo lekani kuchitira naye zinthu limodzi,+ kuti achite manyazi.+
5 muzitulutsira mwamuna kapena mkazi wochita chinthu choipayo kunja kwa mzinda, ndipo muzim’ponya miyala kuti afe.+
17 Tsopano ndikukudandaulirani abale, kuti musamale ndi anthu amene amayambitsa magawano+ ndi kuchita zinthu zokhumudwitsa ena. Zimenezi ndi zosemphana ndi chiphunzitso+ chimene munaphunzira, choncho muziwapewa.+
11 Koma tsopano ndikukulemberani kuti muleke kuyanjana+ ndi aliyense wotchedwa m’bale, amene ndi wadama, kapena waumbombo,+ kapena wopembedza mafano, wolalata, chidakwa,+ kapena wolanda, ngakhale kudya naye munthu wotereyu ayi.
6 Tsopano tikukulangizani+ abale m’dzina la Ambuye Yesu Khristu, kuti mupewe+ m’bale aliyense woyenda mosalongosoka+ komanso mosagwirizana ndi mwambo umene tinakupatsani.+
14 Koma ngati wina sakumvera mawu athu+ a m’kalatayi, muikeni chizindikiro+ ndipo lekani kuchitira naye zinthu limodzi,+ kuti achite manyazi.+