Aroma 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano ndikukudandaulirani abale, kuti musamale ndi anthu amene amayambitsa magawano+ ndi kuchita zinthu zokhumudwitsa ena. Zimenezi ndi zosemphana ndi chiphunzitso+ chimene munaphunzira, choncho muziwapewa.+ 1 Akorinto 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma tsopano ndikukulemberani kuti muleke kuyanjana+ ndi aliyense wotchedwa m’bale, amene ndi wadama, kapena waumbombo,+ kapena wopembedza mafano, wolalata, chidakwa,+ kapena wolanda, ngakhale kudya naye munthu wotereyu ayi. Tito 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu wolimbikitsa mpatuko,+ usagwirizane+ nayenso utamudzudzula koyamba ndi kachiwiri,+ 2 Yohane 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wina akabwera kwa inu ndi chiphunzitso chosiyana ndi ichi, musamulandire m’nyumba zanu+ kapena kumupatsa moni.+
17 Tsopano ndikukudandaulirani abale, kuti musamale ndi anthu amene amayambitsa magawano+ ndi kuchita zinthu zokhumudwitsa ena. Zimenezi ndi zosemphana ndi chiphunzitso+ chimene munaphunzira, choncho muziwapewa.+
11 Koma tsopano ndikukulemberani kuti muleke kuyanjana+ ndi aliyense wotchedwa m’bale, amene ndi wadama, kapena waumbombo,+ kapena wopembedza mafano, wolalata, chidakwa,+ kapena wolanda, ngakhale kudya naye munthu wotereyu ayi.
10 Wina akabwera kwa inu ndi chiphunzitso chosiyana ndi ichi, musamulandire m’nyumba zanu+ kapena kumupatsa moni.+