1 Akorinto 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti payeneradi kukhala magulu ampatuko+ pakati panu, kuti anthu ovomerezedwa aonekere pakati panu.+ Chivumbulutso 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komabe, pali chinthu chimodzi chimene ukuchita bwino: Umadana+ ndi ntchito za mpatuko wa Nikolao,+ zimenenso ine ndimadana nazo.
19 Pakuti payeneradi kukhala magulu ampatuko+ pakati panu, kuti anthu ovomerezedwa aonekere pakati panu.+
6 Komabe, pali chinthu chimodzi chimene ukuchita bwino: Umadana+ ndi ntchito za mpatuko wa Nikolao,+ zimenenso ine ndimadana nazo.