Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 20:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndipo pakati panu anthu ena adzayamba kulankhula zinthu zopotoka+ kuti apatutse ophunzira aziwatsatira.+

  • 1 Akorinto 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndikutanthauza kuti, ena mwa inu amanena kuti: “Ine ndine wa Paulo,” ena amati, “Ine ndine wa Apolo,”+ enanso amati “Ine ndine wa Kefa,” pamene ena amati, “Ine ndine wa Khristu.”

  • Agalatiya 5:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 kupembedza mafano, kuchita zamizimu,+ udani, ndewu, nsanje, kupsa mtima, mikangano, kugawikana, magulu ampatuko,

  • 1 Timoteyo 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Komabe, mawu ouziridwa amanenadi kuti m’nthawi zam’tsogolo,+ ena adzagwa+ pa chikhulupiriro, chifukwa chomvetsera mawu ouziridwa omwe ndi osocheretsa,+ ndiponso ziphunzitso za ziwanda.+

  • 2 Petulo 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Komabe, pakati pa anthuwo panadzakhala aneneri onyenga. Momwemonso padzakhala aphunzitsi onyenga pakati panu.+ Amenewa adzabweretsa mwakachetechete timagulu tampatuko towononga ndipo adzakana ngakhale iye amene anawagula,+ n’kudzibweretsera chiwonongeko chofulumira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena