Agalatiya 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu ena akuyesetsa kwambiri kuti akukopereni kwa iwowo,+ osati ndi zolinga zabwino, koma kuti akutsekerezeni kuti musabwere kwa ine, kuti inuyo muyesetse kuwatsatira.+ 1 Timoteyo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe, mawu ouziridwa amanenadi kuti m’nthawi zam’tsogolo,+ ena adzagwa+ pa chikhulupiriro, chifukwa chomvetsera mawu ouziridwa omwe ndi osocheretsa,+ ndiponso ziphunzitso za ziwanda.+ 1 Yohane 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amenewo anachoka pakati pathu, koma sanali m’gulu lathu,+ chifukwa akanakhala a m’gulu lathu, akanakhalabe ndi ife.+ Sikuti onse ali m’gulu lathu ayi, ndipo iwo achoka m’gulu lathu, kuti zimenezi zidziwike.+
17 Anthu ena akuyesetsa kwambiri kuti akukopereni kwa iwowo,+ osati ndi zolinga zabwino, koma kuti akutsekerezeni kuti musabwere kwa ine, kuti inuyo muyesetse kuwatsatira.+
4 Komabe, mawu ouziridwa amanenadi kuti m’nthawi zam’tsogolo,+ ena adzagwa+ pa chikhulupiriro, chifukwa chomvetsera mawu ouziridwa omwe ndi osocheretsa,+ ndiponso ziphunzitso za ziwanda.+
19 Amenewo anachoka pakati pathu, koma sanali m’gulu lathu,+ chifukwa akanakhala a m’gulu lathu, akanakhalabe ndi ife.+ Sikuti onse ali m’gulu lathu ayi, ndipo iwo achoka m’gulu lathu, kuti zimenezi zidziwike.+