Machitidwe 20:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndipo pakati panu anthu ena adzayamba kulankhula zinthu zopotoka+ kuti apatutse ophunzira aziwatsatira.+ Afilipi 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti ena onse akungofuna za iwo eni,+ osati za Khristu Yesu.
30 Ndipo pakati panu anthu ena adzayamba kulankhula zinthu zopotoka+ kuti apatutse ophunzira aziwatsatira.+