17 Anthu ena akuyesetsa kwambiri kuti akukopereni kwa iwowo,+ osati ndi zolinga zabwino, koma kuti akutsekerezeni kuti musabwere kwa ine, kuti inuyo muyesetse kuwatsatira.+
10 Pakuti Dema+ wandisiya chifukwa chokonda zinthu za m’nthawi* ino,+ ndipo wapita ku Tesalonika. Keresike wapita ku Galatiya,+ ndipo Tito wapita ku Dalimatiya.