Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 10:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 monga mmene ineyo ndikukondweretsera anthu onse m’zinthu zonse.+ Sikuti ndikungofuna zopindulitsa ine ndekha ayi,+ koma zopindulitsa anthu ambiri, kuti apulumutsidwe.+

  • 1 Akorinto 13:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 sichichita zosayenera,+ sichisamala zofuna zake zokha,+ sichikwiya.+ Sichisunga zifukwa.+

  • Afilipi 2:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pakuti ena onse akungofuna za iwo eni,+ osati za Khristu Yesu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena