1 Atesalonika 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Akutero pamene akuyesa kutiletsa+ kulankhula kwa anthu a mitundu ina kuti angapulumutsidwe.+ Chotsatira chake n’chakuti, pochita zimenezi nthawi zonse akudzazitsa+ machimo awo. Koma tsopano mkwiyo wake wawafikira.+
16 Akutero pamene akuyesa kutiletsa+ kulankhula kwa anthu a mitundu ina kuti angapulumutsidwe.+ Chotsatira chake n’chakuti, pochita zimenezi nthawi zonse akudzazitsa+ machimo awo. Koma tsopano mkwiyo wake wawafikira.+