Aroma 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aliyense wa ife azikondweretsa mnzake pa zinthu zabwino zomulimbikitsa.+ Afilipi 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musamaganizire zofuna zanu zokha,+ koma muziganiziranso zofuna za ena.+