1 Akorinto 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kwa ofooka ndinakhala wofooka, kuti ndipindule ofooka.+ Ndakhala zinthu zonse kwa anthu osiyanasiyana,+ kuti mulimonse mmene zingakhalire ndipulumutseko ena. Afilipi 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musamaganizire zofuna zanu zokha,+ koma muziganiziranso zofuna za ena.+
22 Kwa ofooka ndinakhala wofooka, kuti ndipindule ofooka.+ Ndakhala zinthu zonse kwa anthu osiyanasiyana,+ kuti mulimonse mmene zingakhalire ndipulumutseko ena.