Aroma 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Landirani munthu wokhala ndi zofooka m’chikhulupiriro+ chake, koma osagamula pa zoganiza za mumtima mwake.+ Aroma 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ife olimba tiyenera kunyamula zofooka za osalimba,+ osati kumadzikondweretsa tokha ayi.+ 2 Akorinto 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndani ali wofooka,+ ine osakhalanso wofooka? Ndani wakhumudwitsidwa, ine osakwiya nazo?
14 Landirani munthu wokhala ndi zofooka m’chikhulupiriro+ chake, koma osagamula pa zoganiza za mumtima mwake.+