Aroma 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ife olimba tiyenera kunyamula zofooka za osalimba,+ osati kumadzikondweretsa tokha ayi.+ 1 Akorinto 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zikatero, ungawononge munthu wofookayo, yemwe ndi m’bale wako amene Khristu anamufera,+ chifukwa chakuti ukudziwa zinthu. 1 Atesalonika 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso tikukudandaulirani abale kuti, langizani ochita zosalongosoka,+ lankhulani molimbikitsa kwa amtima wachisoni,+ thandizani ofooka, khalani oleza+ mtima kwa onse.
11 Zikatero, ungawononge munthu wofookayo, yemwe ndi m’bale wako amene Khristu anamufera,+ chifukwa chakuti ukudziwa zinthu.
14 Komanso tikukudandaulirani abale kuti, langizani ochita zosalongosoka,+ lankhulani molimbikitsa kwa amtima wachisoni,+ thandizani ofooka, khalani oleza+ mtima kwa onse.