1 Akorinto 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Aliyense asamangodzifunira zopindulitsa iye yekha basi,+ koma zopindulitsanso wina.+ Afilipi 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musamaganizire zofuna zanu zokha,+ koma muziganiziranso zofuna za ena.+