Machitidwe 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano Myuda wina dzina lake Apolo,+ mbadwa ya ku Alekizandiriya, amene anali ndi mphatso ya kulankhula, anafika ku Efeso. Iyeyu analinso kuwadziwa bwino Malemba.+ 1 Akorinto 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngati wina akunena kuti: “Ine ndine wa Paulo,” ndipo wina akunenanso kuti: “Ine ndine wa Apolo,”+ kodi sindiye kuti mukungofanana ndi anthu onse basi? 1 Akorinto 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chotero pasakhale munthu wodzitama chifukwa cha anthu, popeza zinthu zonse ndi zanu,+
24 Tsopano Myuda wina dzina lake Apolo,+ mbadwa ya ku Alekizandiriya, amene anali ndi mphatso ya kulankhula, anafika ku Efeso. Iyeyu analinso kuwadziwa bwino Malemba.+
4 Ngati wina akunena kuti: “Ine ndine wa Paulo,” ndipo wina akunenanso kuti: “Ine ndine wa Apolo,”+ kodi sindiye kuti mukungofanana ndi anthu onse basi?