Machitidwe 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nthawi inayake, Apolo+ ali ku Korinto, Paulo anadzera kumadera a kumtunda mpaka anafika ku Efeso.+ Kumeneko anapezako ophunzira ena, 1 Akorinto 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndikutanthauza kuti, ena mwa inu amanena kuti: “Ine ndine wa Paulo,” ena amati, “Ine ndine wa Apolo,”+ enanso amati “Ine ndine wa Kefa,” pamene ena amati, “Ine ndine wa Khristu.” 1 Akorinto 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ineyo ndinabzala,+ Apolo anathirira,+ koma Mulungu ndiye anakulitsa.+
19 Nthawi inayake, Apolo+ ali ku Korinto, Paulo anadzera kumadera a kumtunda mpaka anafika ku Efeso.+ Kumeneko anapezako ophunzira ena,
12 Ndikutanthauza kuti, ena mwa inu amanena kuti: “Ine ndine wa Paulo,” ena amati, “Ine ndine wa Apolo,”+ enanso amati “Ine ndine wa Kefa,” pamene ena amati, “Ine ndine wa Khristu.”