Machitidwe 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano Myuda wina dzina lake Apolo,+ mbadwa ya ku Alekizandiriya, amene anali ndi mphatso ya kulankhula, anafika ku Efeso. Iyeyu analinso kuwadziwa bwino Malemba.+ 1 Akorinto 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi Apolo ndani?+ Inde, Paulo ndani? Iwo angokhala atumiki+ amene anakuthandizani kukhala okhulupirira, malinga ndi ntchito imene Ambuye anagawira aliyense wa iwo.
24 Tsopano Myuda wina dzina lake Apolo,+ mbadwa ya ku Alekizandiriya, amene anali ndi mphatso ya kulankhula, anafika ku Efeso. Iyeyu analinso kuwadziwa bwino Malemba.+
5 Kodi Apolo ndani?+ Inde, Paulo ndani? Iwo angokhala atumiki+ amene anakuthandizani kukhala okhulupirira, malinga ndi ntchito imene Ambuye anagawira aliyense wa iwo.