1 Akorinto 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti payeneradi kukhala magulu ampatuko+ pakati panu, kuti anthu ovomerezedwa aonekere pakati panu.+ Chivumbulutso 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiponso uli ndi olimbikira chiphunzitso cha mpatuko wa Nikolao.+
19 Pakuti payeneradi kukhala magulu ampatuko+ pakati panu, kuti anthu ovomerezedwa aonekere pakati panu.+