Miyambo 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakamwa pa munthu wopusa m’pamene pamamuwononga,+ ndipo milomo yake ndi msampha wa moyo wake.+ Luka 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye anamuuza kuti, ‘Ndikuweruza mwa zotuluka pakamwa pako,+ kapolo woipa iwe. Ukuti unadziwa kuti ine ndine munthu wouma mtima, wotenga zimene sindinasungitse ndi kukolola zimene sindinafese?+
22 Iye anamuuza kuti, ‘Ndikuweruza mwa zotuluka pakamwa pako,+ kapolo woipa iwe. Ukuti unadziwa kuti ine ndine munthu wouma mtima, wotenga zimene sindinasungitse ndi kukolola zimene sindinafese?+