Luka 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye anamuuza kuti, ‘Ndikuweruza potengera zimene wanena, kapolo woipa iwe. Ukuti umadziwa kuti ine ndine munthu wouma mtima, wotenga zimene sindinasungitse ndi kukolola zimene sindinafese.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:22 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 232-233 Nsanja ya Olonda,10/1/1989, ptsa. 8-9
22 Iye anamuuza kuti, ‘Ndikuweruza potengera zimene wanena, kapolo woipa iwe. Ukuti umadziwa kuti ine ndine munthu wouma mtima, wotenga zimene sindinasungitse ndi kukolola zimene sindinafese.+