Luka 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye anamuuza kuti, ‘Ndikuweruza mwa zotuluka pakamwa pako,+ kapolo woipa iwe. Ukuti unadziwa kuti ine ndine munthu wouma mtima, wotenga zimene sindinasungitse ndi kukolola zimene sindinafese?+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:22 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 232-233 Nsanja ya Olonda,10/1/1989, ptsa. 8-9
22 Iye anamuuza kuti, ‘Ndikuweruza mwa zotuluka pakamwa pako,+ kapolo woipa iwe. Ukuti unadziwa kuti ine ndine munthu wouma mtima, wotenga zimene sindinasungitse ndi kukolola zimene sindinafese?+