2 Samueli 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Davide anamuuza kuti: “Mlandu wa magazi ako ukhale pamutu pako,+ chifukwa wadzichitira wekha umboni+ ponena kuti, ‘Ineyo ndapha wodzozedwa wa Yehova.’”+ Mateyu 12:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pakuti ndi mawu ako udzaweruzidwa kuti ndiwe wolungama, ndipo ndi mawu akonso udzaweruzidwa kuti ndiwe wolakwa.”+
16 Kenako Davide anamuuza kuti: “Mlandu wa magazi ako ukhale pamutu pako,+ chifukwa wadzichitira wekha umboni+ ponena kuti, ‘Ineyo ndapha wodzozedwa wa Yehova.’”+
37 Pakuti ndi mawu ako udzaweruzidwa kuti ndiwe wolungama, ndipo ndi mawu akonso udzaweruzidwa kuti ndiwe wolakwa.”+