Miyambo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mboni yonama sidzalephera kulangidwa,+ ndipo wolankhula mabodza sadzapulumuka.+ Miyambo 21:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mboni yonama idzawonongedwa,+ koma munthu amene amamvetsera adzalankhula kwamuyaya.+